MUSAWONONGE

NDIFE NDANI?

Musawononge ndi bungwe lodziwako pang'ono zinthu zokhudzana ndi za umoyo, za nyumba, za magalimoto ndi za bongogetsi.

Pofuna kukuthandizani kuti mumvetsetse zomwe tidzilemba tiyika m'ndondomeko wa mawu wofotokozela mawu a chichewa omwe timawadziwa ndiponso omwe tidzigwilitsa nthito pa chinkokano chino. Komanso muli ndi mwayi woti mungathe kufunsa kapena kupeleka maganizo anu pa zomwe zili pa chinkokanochi. Maganizo anu ali olandilidwa nthawi zonse.

Cholinga chathu ndi kukuthandizani mu zina ndi zina zokhudzana ndi magawo omwe ife tikudziwapo kanthu monga momwe tafotokozela pamwambapa.

Sankhani tsamba lomwe mukufuna kupita pansipa.